Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Esitere 5:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Ndiyeno Hamani anayamba kudzitamandira pamaso pawo chifukwa cha kuchuluka kwa chuma chake+ ndi kuchuluka kwa ana ake aamuna.+ Anadzitamandiranso chifukwa cha zonse zimene mfumu inamulemekeza nazo komanso chifukwa chakuti inamukweza kuposa akalonga ndi atumiki a mfumu.+

  • Yeremiya 9:23
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 23 Yehova wanena kuti: “Munthu wanzeru asadzitamande chifukwa cha nzeru zake.+ Munthu wamphamvu asadzitamande chifukwa cha mphamvu zake.+ Munthu wachuma asadzitamande chifukwa cha chuma chake.”+

  • Luka 12:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Ndipo ndidzauza+ moyo wanga kuti: “Moyo wangawe, uli ndi zinthu zambiri zabwino mwakuti zisungika kwa zaka zambiri. Ungoti phee tsopano, ndipo udye, umwe ndi kusangalala.”’+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena