Esitere 9:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 ana aamuna 10+ a Hamani+ mwana wa Hamedata amene anali kudana ndi Ayuda.+ Ayuda anapha amuna amenewa koma sanafunkhe+ zinthu zawo. Yobu 27:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Ana ake akachuluka, amachulukira lupanga.+Mbadwa zake sizidzakhala ndi chakudya chokwanira.
10 ana aamuna 10+ a Hamani+ mwana wa Hamedata amene anali kudana ndi Ayuda.+ Ayuda anapha amuna amenewa koma sanafunkhe+ zinthu zawo.