Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Deuteronomo 8:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Samalani kuti munganene mumtima mwanu kuti, ‘Chuma ichi ndachipeza ndi mphamvu zanga ndi nyonga za dzanja langa.’+

  • Salimo 52:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  7 Munthu wamphamvu wotere sadalira Mulungu monga malo ake achitetezo,+

      Koma amadalira kuchuluka kwa chuma chake,+

      Ndipo chitetezo chake amachipeza m’mavuto amene iyeyo amawachititsa.+

  • Miyambo 10:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Zinthu zamtengo wapatali za munthu wachuma zili ngati mudzi wake wolimba.+ Chiwonongeko cha onyozeka ndicho umphawi wawo.+

  • Miyambo 18:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Zinthu zamtengo wapatali za munthu wachuma ndizo mzinda wake wolimba,+ ndipo m’maganizo mwake zili ngati mpanda woteteza.+

  • 1 Timoteyo 6:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Lamula achuma+ a m’nthawi* ino kuti asakhale odzikweza,+ ndiponso kuti asamadalire chuma chosadalirika,+ koma adalire Mulungu, amene amatipatsa mowolowa manja zinthu zonse kuti tisangalale.+

  • 1 Yohane 2:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Pakuti chilichonse cha m’dziko,+ monga chilakolako cha thupi,+ chilakolako cha maso+ ndi kudzionetsera ndi zimene munthu ali nazo pa moyo wake,+ sizichokera kwa Atate, koma kudziko.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena