Genesis 3:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Mkaziyo atamva zimenezo, anayamba kuona kuti zipatso za mtengowo n’zokoma kudya, zokhumbirika ndi zosiririka.+ Choncho anathyola chipatso cha mtengowo n’kudya. Pambuyo pake, anapatsako mwamuna wake pamene anali limodzi, ndipo nayenso anadya.+ Miyambo 27:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Manda ndiponso malo a chiwonongeko+ sakhuta.+ Nawonso maso a munthu sakhuta.+ Mateyu 4:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ndiyeno Mdyerekezi anamutenganso ndi kupita naye paphiri lalitali kwambiri, ndipo anamuonetsa maufumu onse a padziko+ ndi ulemerero wawo.
6 Mkaziyo atamva zimenezo, anayamba kuona kuti zipatso za mtengowo n’zokoma kudya, zokhumbirika ndi zosiririka.+ Choncho anathyola chipatso cha mtengowo n’kudya. Pambuyo pake, anapatsako mwamuna wake pamene anali limodzi, ndipo nayenso anadya.+
8 Ndiyeno Mdyerekezi anamutenganso ndi kupita naye paphiri lalitali kwambiri, ndipo anamuonetsa maufumu onse a padziko+ ndi ulemerero wawo.