Mlaliki 5:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Zinthu zabwino zikachuluka ozidya amachulukanso,+ ndipo kodi mwiniwake wa zinthuzo amapindula chiyani kuposa kumangoziyang’ana ndi maso ake?+ Yakobo 4:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Koma tsopano mumakonda kudzitama.+ Kunyada konse koteroko ndi koipa.
11 Zinthu zabwino zikachuluka ozidya amachulukanso,+ ndipo kodi mwiniwake wa zinthuzo amapindula chiyani kuposa kumangoziyang’ana ndi maso ake?+