-
Yesaya 39:2Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
2 Chotero Hezekiya anasangalala ndi alendowo+ ndipo anawaonetsa nyumba yake yosungiramo chuma.+ Anawaonetsa siliva, golide, mafuta a basamu,+ mafuta abwino, zonse za m’nyumba yake yosungiramo zida zankhondo,+ ndi chuma chake chonse. Palibe chimene Hezekiya sanawaonetse m’nyumba yake+ ndi mu ufumu wake wonse.+
-