Nehemiya 3:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Ndiyeno Ezeri mwana wamwamuna wa Yesuwa,+ kalonga wa Mizipa,+ anakonza gawo lina la mpandawo pafupi ndi chikweza chimene anthu amadutsa popita Kosungira Zida pa Mchirikizo wa Khoma.+ Yesaya 22:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 ndipo wina adzachotsa chophimba cha Yuda. M’tsiku limenelo, udzayang’ana kunyumba ya nkhalango yosungiramo zida zankhondo.+
19 Ndiyeno Ezeri mwana wamwamuna wa Yesuwa,+ kalonga wa Mizipa,+ anakonza gawo lina la mpandawo pafupi ndi chikweza chimene anthu amadutsa popita Kosungira Zida pa Mchirikizo wa Khoma.+
8 ndipo wina adzachotsa chophimba cha Yuda. M’tsiku limenelo, udzayang’ana kunyumba ya nkhalango yosungiramo zida zankhondo.+