-
Nehemiya 3:15Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
15 Saluni mwana wamwamuna wa Kolihoze, kalonga wa chigawo cha Mizipa,+ anakonza Chipata cha Kukasupe.+ Iye anachimanga ndi kukhoma denga* lake. Anaikanso zitseko zake,+ akapichi ake ndi mipiringidzo yake. Iye anamanganso mpanda wa Dziwe+ la Ngalande* kukafika ku Munda wa Mfumu+ ndi ku Masitepe+ ochokera ku Mzinda wa Davide.+
-