Ezara 2:40 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 40 Alevi:+ Ana a Yesuwa,+ a m’nyumba ya Kadimiyeli+ ochokera pakati pa ana a Hodaviya,+ 74. Nehemiya 10:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Panalinso Alevi awa amene anatsimikizira panganoli: Yesuwa,+ mwana wamwamuna wa Azaniya, Binui wochokera pakati pa ana a Henadadi,+ Kadimiyeli,
9 Panalinso Alevi awa amene anatsimikizira panganoli: Yesuwa,+ mwana wamwamuna wa Azaniya, Binui wochokera pakati pa ana a Henadadi,+ Kadimiyeli,