Ezara 3:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Chotero Yesuwa,+ ana ake ndi abale ake, Kadimiyeli ndi ana ake, ndi ana a Yuda,* ananyamuka monga gulu limodzi kukayang’anira anthu ogwira ntchito m’nyumba ya Mulungu woona. Komanso panali ana a Henadadi,+ ana awo ndi abale awo, omwe anali Alevi.
9 Chotero Yesuwa,+ ana ake ndi abale ake, Kadimiyeli ndi ana ake, ndi ana a Yuda,* ananyamuka monga gulu limodzi kukayang’anira anthu ogwira ntchito m’nyumba ya Mulungu woona. Komanso panali ana a Henadadi,+ ana awo ndi abale awo, omwe anali Alevi.