-
Nehemiya 3:18Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
18 Abale awo anakonza mpandawo kuchokera pamenepo moyang’aniridwa ndi Bavai mwana wamwamuna wa Henadadi, kalonga wa hafu ya chigawo cha Keila.
-