1 Samueli 14:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Ndiyeno anthu onse a m’dzikomo anapita kunkhalango, pa nthawi imene uchi+ unali pena paliponse kutchireko. Miyambo 25:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Ukapeza uchi udye wokukwanira,+ kuti usadye wambiri n’kuusanza.+ Mateyu 3:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Koma Yohane ameneyu, anali kuvala chovala chaubweya wa ngamila+ ndi lamba wachikopa+ m’chiuno mwake. Chakudya chake chinali dzombe+ ndi uchi.+
25 Ndiyeno anthu onse a m’dzikomo anapita kunkhalango, pa nthawi imene uchi+ unali pena paliponse kutchireko.
4 Koma Yohane ameneyu, anali kuvala chovala chaubweya wa ngamila+ ndi lamba wachikopa+ m’chiuno mwake. Chakudya chake chinali dzombe+ ndi uchi.+