1 Samueli 14:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Koma Yonatani sanamve pamene bambo ake analumbirira anthu.+ Chotero anatambasula dzanja lake ndi kukhudza chisa cha uchi ndi ndodo. Kenako ananyambita ndodoyo, ndipo atatero, anayera m’maso.+ Miyambo 24:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Mwana wanga, idya uchi chifukwa ndi wabwino, ndipo uchi wotsekemera wochokera pazisa za njuchi uuike m’kamwa mwako.+
27 Koma Yonatani sanamve pamene bambo ake analumbirira anthu.+ Chotero anatambasula dzanja lake ndi kukhudza chisa cha uchi ndi ndodo. Kenako ananyambita ndodoyo, ndipo atatero, anayera m’maso.+
13 Mwana wanga, idya uchi chifukwa ndi wabwino, ndipo uchi wotsekemera wochokera pazisa za njuchi uuike m’kamwa mwako.+