-
Nyimbo ya Solomo 5:1Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
5 “Ndabwera m’munda mwanga,+ iwe mlongo wanga,+ mkwatibwi wanga.+ Ndathyola mule+ wanga limodzi ndi zonunkhiritsa zanga. Ndadya chisa changa cha uchi limodzi ndi uchi wanga.+ Ndamwa vinyo wanga limodzi ndi mkaka wanga.”
“Idyani, inu anthu okondana! Imwani ndipo muledzere ndi chikondi chimene mukusonyezana.”+
-