Oweruza 14:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Patapita nthawi, Samisoni anabwerera kwa mkaziyo kuti akam’tenge ndi kupita naye kwawo.+ Ali m’njira, anapatuka kuti aone mkango umene anapha uja. Atafika pamene anaphera mkango paja anapeza kuti m’thupi la mkango wakufa uja muli njuchi ndi uchi.+ Miyambo 24:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Mwana wanga, idya uchi chifukwa ndi wabwino, ndipo uchi wotsekemera wochokera pazisa za njuchi uuike m’kamwa mwako.+
8 Patapita nthawi, Samisoni anabwerera kwa mkaziyo kuti akam’tenge ndi kupita naye kwawo.+ Ali m’njira, anapatuka kuti aone mkango umene anapha uja. Atafika pamene anaphera mkango paja anapeza kuti m’thupi la mkango wakufa uja muli njuchi ndi uchi.+
13 Mwana wanga, idya uchi chifukwa ndi wabwino, ndipo uchi wotsekemera wochokera pazisa za njuchi uuike m’kamwa mwako.+