-
Mateyu 1:24Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
24 Ndiyeno Yosefe anadzuka ndi kuchita mmene mngelo wa Yehova anamulangizira. Anatenga mkazi wake ndi kupita naye kunyumba.
-