1 Samueli 31:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Chotero Sauli, ana ake atatu, ndi womunyamulira zida komanso asilikali ake onse, anafera limodzi pa tsiku limenelo.+ 1 Mbiri 10:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Chotero Sauli ndi ana ake atatu anafa,+ ndipo anthu onse a m’nyumba yake anafera limodzi.
6 Chotero Sauli, ana ake atatu, ndi womunyamulira zida komanso asilikali ake onse, anafera limodzi pa tsiku limenelo.+