Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 2 Mafumu 7:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Tsopano anthu anapita kukafunkha+ msasa wa Asiriya. Choncho ufa wosalala wokwana muyezo umodzi wa seya, mtengo wake unafika pa sekeli imodzi, ndipo balere wokwana miyezo iwiri ya seya, mtengo wake unafikanso pa sekeli imodzi, mogwirizana ndi mawu+ a Yehova.

  • 2 Mbiri 14:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Asa ndi anthu amene anali naye anawathamangitsa mpaka kukafika ku Gerari,+ ndipo Aitiyopiyawo anapitiriza kuphedwa mpaka palibe amene anatsala ndi moyo, popeza Yehova+ ndi gulu lake+ anawagonjetseratu. Pambuyo pake, anthuwo anatenga zofunkha zochuluka zedi.+

  • 2 Mbiri 20:25
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 25 Choncho Yehosafati ndi anthu ake anapita kukafunkha+ zinthu zimene adaniwo anali nazo. Iwo anapeza zinthu zochuluka pakati pa anthuwo monga katundu wosiyanasiyana, zovala ndi zinthu zina zabwinozabwino. Chotero anayamba kutenga zinthuzo mpaka zinawakanika kunyamula.+ Kwa masiku atatu anakhala akututa zofunkhazo chifukwa zinalipo zambiri.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena