Ekisodo 12:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Ndipo ana a Isiraeli anachita mogwirizana ndi mawu onse amene Mose anawauza, motero anapempha Aiguputo zinthu zasiliva, zagolide ndi zovala.+ 2 Mafumu 7:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Anthuwo anatsatira Asiriyawo mpaka kukafika ku Yorodano, ndipo m’njira monsemo munali zovala ndi ziwiya+ zimene Asiriyawo anataya pothawa.+ Kenako anthuwo anabwerera n’kukanena kwa mfumu. Miyambo 13:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Munthu wabwino adzasiyira cholowa zidzukulu zake, ndipo chuma cha wochimwa chimasungidwa kuti chidzakhale cha munthu wolungama.+
35 Ndipo ana a Isiraeli anachita mogwirizana ndi mawu onse amene Mose anawauza, motero anapempha Aiguputo zinthu zasiliva, zagolide ndi zovala.+
15 Anthuwo anatsatira Asiriyawo mpaka kukafika ku Yorodano, ndipo m’njira monsemo munali zovala ndi ziwiya+ zimene Asiriyawo anataya pothawa.+ Kenako anthuwo anabwerera n’kukanena kwa mfumu.
22 Munthu wabwino adzasiyira cholowa zidzukulu zake, ndipo chuma cha wochimwa chimasungidwa kuti chidzakhale cha munthu wolungama.+