Genesis 15:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Koma mtundu umene adzautumikirewo ndidzauweruza.+ Pambuyo pake, iwo adzachokako ndi katundu wochuluka.+ Ekisodo 3:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Chotero ndidzachititsa Aiguputo kukomera mtima anthu anga, moti pochoka simudzachoka chimanjamanja.+ Ekisodo 11:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Tsopano uza anthu kuti mwamuna aliyense ndi mkazi aliyense apemphe kwa mnzake zinthu zasiliva ndi zagolide.”+ Salimo 105:37 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 37 Ndiyeno anayamba kuwatulutsa atatenga siliva ndi golide.+Pakati pa mafuko ake panalibe amene anapunthwa panjira.
14 Koma mtundu umene adzautumikirewo ndidzauweruza.+ Pambuyo pake, iwo adzachokako ndi katundu wochuluka.+
21 Chotero ndidzachititsa Aiguputo kukomera mtima anthu anga, moti pochoka simudzachoka chimanjamanja.+
2 Tsopano uza anthu kuti mwamuna aliyense ndi mkazi aliyense apemphe kwa mnzake zinthu zasiliva ndi zagolide.”+
37 Ndiyeno anayamba kuwatulutsa atatenga siliva ndi golide.+Pakati pa mafuko ake panalibe amene anapunthwa panjira.