Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Esitere 1:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Anthu anali kulandira vinyo m’ziwiya zagolide.+ Chiwiya chilichonse chinali chosiyana ndi chinzake, ndipo vinyo amene mfumu inapereka+ anali wochuluka kwambiri, moti ndi mfumu yokha imene ikanatha kupereka vinyo wochuluka choncho.

  • Yesaya 22:24
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 24 Anthu adzapachika pa iyeyo ulemerero wonse wa nyumba ya bambo ake: mbadwa ndi mphukira, kutanthauza mitundu yonse ya ziwiya zing’onozing’ono, mitundu yonse ya ziwiya zolowa, ndi mitundu yonse ya mitsuko ikuluikulu.’

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena