Genesis 37:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Iwo anamuonera patali akubwera, ndipo asanafike pafupi anayamba kupangana chiwembu choti amuphe.+ Salimo 64:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Amafunafuna kuchita zinthu zosalungama,+Abisa chiwembu chimene achikonza mochenjera,+Ndipo zamkati, zamumtima mwa aliyense, n’zovuta kuzimvetsa.+ Miyambo 6:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Maso odzikweza,+ lilime lonama,+ manja okhetsa magazi a anthu osalakwa,+
6 Amafunafuna kuchita zinthu zosalungama,+Abisa chiwembu chimene achikonza mochenjera,+Ndipo zamkati, zamumtima mwa aliyense, n’zovuta kuzimvetsa.+