Ekisodo 2:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Monga mwa masiku onse, abusa anafika ndi kuwachotsapo atsikanawo. Zitatero Mose ananyamuka ndi kuthandiza atsikanawo, ndipo iye anamwetsa ziweto zawo.+
17 Monga mwa masiku onse, abusa anafika ndi kuwachotsapo atsikanawo. Zitatero Mose ananyamuka ndi kuthandiza atsikanawo, ndipo iye anamwetsa ziweto zawo.+