Deuteronomo 24:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 “Mwamuna akatenga mkazi watsopano,+ sayenera kukhala m’gulu lankhondo, ndiponso asakakamizidwe kuchita china chilichonse. Akhale kunyumba osachita zinthu zimenezi kwa chaka chimodzi kuti asangalatse mkazi amene watenga.+ Salimo 19:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Dzuwalo limaoneka ngati mkwati amene akutuluka m’chipinda chake,+Limakondwa ngati mmene mwamuna wamphamvu amachitira akamathamanga m’njira.+
5 “Mwamuna akatenga mkazi watsopano,+ sayenera kukhala m’gulu lankhondo, ndiponso asakakamizidwe kuchita china chilichonse. Akhale kunyumba osachita zinthu zimenezi kwa chaka chimodzi kuti asangalatse mkazi amene watenga.+
5 Dzuwalo limaoneka ngati mkwati amene akutuluka m’chipinda chake,+Limakondwa ngati mmene mwamuna wamphamvu amachitira akamathamanga m’njira.+