Genesis 30:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Koma Labani anauza Yakobo kuti: “Ngati wandikomera mtima, ungokhala konkuno. Ndaombeza maula ndipo ndapeza kuti Yehova akundidalitsa chifukwa cha iwe.”+ 1 Samueli 18:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Kuyambira tsiku limenelo, Sauli anayamba kuyang’ana Davide ndi diso loipa.+
27 Koma Labani anauza Yakobo kuti: “Ngati wandikomera mtima, ungokhala konkuno. Ndaombeza maula ndipo ndapeza kuti Yehova akundidalitsa chifukwa cha iwe.”+