-
Genesis 30:32Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
32 Ine ndipita kukayenda pakati pa ziweto zanu zonse lero. Inuyo mukapatule nkhosa iliyonse yamathothomathotho kapena yamawangamawanga, ndi nkhosa iliyonse yaing’ono yamphongo yofiirira, ndi mbuzi iliyonse yaikazi yamawangamawanga kapena yamathothomathotho. Ngati ziweto zoterozo zidzabadwe pambuyo pake, ndizo zidzakhale malipiro anga.+
-