Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 2:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Yehova Mulungu anali kuumba ndi dothi nyama iliyonse yakutchire, ndi cholengedwa chilichonse chouluka m’mlengalenga. Ndipo anayamba kuzibweretsa kwa munthuyo, kuti chilichonse achitche dzina. Dzina lililonse limene munthuyo anatchula chamoyo chilichonse,+ limenelo linakhaladi dzina lake.+

  • Genesis 4:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Kenako Adamu anagona ndi Hava mkazi wake, ndipo mkaziyo anatenga pakati.+ M’kupita kwa nthawi, mkaziyo anabereka Kaini*+ n’kunena kuti: “Ndabereka mwana wamwamuna ndi thandizo la Yehova.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena