Genesis 4:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Kenako Adamu anagona ndi mkazi wake Hava ndipo mkaziyo anakhala woyembekezera.+ Mkaziyo atabereka Kaini*+ ananena kuti: “Ndabereka mwana wamwamuna mothandizidwa ndi Yehova.” Genesis Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 4:1 Nsanja ya Olonda,1/1/2013, tsa. 13 Tsanzirani, ptsa. 10-11 Mawu a Mulungu, tsa. 151
4 Kenako Adamu anagona ndi mkazi wake Hava ndipo mkaziyo anakhala woyembekezera.+ Mkaziyo atabereka Kaini*+ ananena kuti: “Ndabereka mwana wamwamuna mothandizidwa ndi Yehova.”