Genesis 35:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Potsirizira pake Yakobo anafika kwa bambo ake Isaki ku Mamure,+ m’dera la Kiriyati-ariba,+ komwe ndi ku Heburoni. Uku n’kumenenso Abulahamu ndi Isaki anakhalako monga alendo.+
27 Potsirizira pake Yakobo anafika kwa bambo ake Isaki ku Mamure,+ m’dera la Kiriyati-ariba,+ komwe ndi ku Heburoni. Uku n’kumenenso Abulahamu ndi Isaki anakhalako monga alendo.+