Miyambo 29:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Wolungama amaganizira za mlandu wa anthu onyozeka.+ Woipa saganizira zimenezo.+ Maliro 3:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Ndi kupotoza chiweruzo cha munthu pa mlandu wake, Yehova savomereza zimenezi.+