Genesis 26:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Koma iwo anayankha kuti: “Ife taona kuti ndithu Yehova ali nawe.+ Choncho tinaganiza zokupempha kuti, ‘Chonde, tiye tilumbirirane,+ iwe ndi ife, ndipo tichite nawe pangano.+ Agalatiya 3:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Abale, ndipereke fanizo mogwirizana ndi zimene zimachitika pakati pa anthu: Pangano likakhazikitsidwa, ngakhale kuti ndi pangano la anthu, palibe angachotsepo kapena kuwonjezerapo mfundo zina.+
28 Koma iwo anayankha kuti: “Ife taona kuti ndithu Yehova ali nawe.+ Choncho tinaganiza zokupempha kuti, ‘Chonde, tiye tilumbirirane,+ iwe ndi ife, ndipo tichite nawe pangano.+
15 Abale, ndipereke fanizo mogwirizana ndi zimene zimachitika pakati pa anthu: Pangano likakhazikitsidwa, ngakhale kuti ndi pangano la anthu, palibe angachotsepo kapena kuwonjezerapo mfundo zina.+