-
Yoswa 22:27Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
27 koma kuti likhale mboni pakati pa ife+ ndi inu ndi mibadwo yobwera pambuyo pathu. Guwalo likhale mboni yakuti tidzatumikira Yehova pamaso pake ndi nsembe zathu zopsereza, nsembe zachiyanjano ndi nsembe zina,+ kuti tsiku lina m’tsogolo ana anu asadzanene kwa ana athu kuti: “Inu mulibe gawo mwa Yehova.”’
-