7 Muzidzawauza kuti, ‘N’chifukwa chakuti madzi a mumtsinje wa Yorodano anadukana pamaso pa likasa la pangano la Yehova.+ Likasalo litadutsa mumtsinje wa Yorodano, madzi a mtsinje wa Yorodanowo anadukana, ndipo miyala imeneyi ndi chikumbutso cha zimenezo kwa ana a Isiraeli mpaka kalekale.’”+