Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Oweruza 11:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Poyankha akulu a ku Giliyadi anauza Yefita kuti: “Yehova amve makambirano athuwa+ ndi kutiweruza ngati sitidzachita zogwirizana ndi mawu ako.”+

  • 1 Samueli 12:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Atatero, iye anawayankha kuti: “Yehova ndi mboni yokutsutsani, ndipo wodzozedwa+ wake ndi mboni lero kuti simunandipeze ndi mlandu uliwonse.”+ Pamenepo iwo anati: “Inde, iyedi ndi mboni.”

  • Malaki 2:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Inu mwanena kuti, ‘Chifukwa chiyani?’+ Chifukwa chakuti Yehova wakudzudzulani popeza kuti aliyense wa inu wachitira zachinyengo mkazi amene anamukwatira ali mnyamata,+ ngakhale kuti iye anali mnzake komanso mkazi wa pangano lake.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena