Genesis 24:60 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 60 Ndiyeno iwo anayamba kudalitsa Rabeka kuti: “Iwe mlongo wathu, ukakhale mayi wa anthu masauzande kuchulukitsa ndi masauzande 10, ndipo mbewu yako ikalande mizinda ya adani awo.”+
60 Ndiyeno iwo anayamba kudalitsa Rabeka kuti: “Iwe mlongo wathu, ukakhale mayi wa anthu masauzande kuchulukitsa ndi masauzande 10, ndipo mbewu yako ikalande mizinda ya adani awo.”+