Genesis 2:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Nthaka ya padziko lapansi inali isanayambe kumera zitsamba ndi zomera zina, chifukwa Yehova Mulungu anali asanagwetse mvula+ padziko lapansi. Panalibenso munthu woti n’kulima nthakayo. Genesis 3:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Udzadya chakudya kuchokera m’thukuta la nkhope yako mpaka utabwerera kunthaka, pakuti n’kumene unatengedwa.+ Popeza ndiwe fumbi, kufumbiko udzabwerera.”+
5 Nthaka ya padziko lapansi inali isanayambe kumera zitsamba ndi zomera zina, chifukwa Yehova Mulungu anali asanagwetse mvula+ padziko lapansi. Panalibenso munthu woti n’kulima nthakayo.
19 Udzadya chakudya kuchokera m’thukuta la nkhope yako mpaka utabwerera kunthaka, pakuti n’kumene unatengedwa.+ Popeza ndiwe fumbi, kufumbiko udzabwerera.”+