Salimo 133:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 133 Taonani! Ndi zabwino komanso zosangalatsa kwambiriAbale akakhala pamodzi mogwirizana!+ Miyambo 6:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 uchite izi mwana wanga kuti udzipulumutse, pakuti wagwa m’manja mwa mnzako:+ Pita ukadzichepetse ndipo ukamuchonderere kwambiri mnzakoyo.+
3 uchite izi mwana wanga kuti udzipulumutse, pakuti wagwa m’manja mwa mnzako:+ Pita ukadzichepetse ndipo ukamuchonderere kwambiri mnzakoyo.+