Genesis 32:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Tsopano ndili ndi ng’ombe, abulu, nkhosa, komanso antchito aamuna ndi aakazi.+ Ndatumiza amithenga kwa mbuyanga kukupemphani kuti mundikomere mtima.”’”+ Genesis 33:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Ndiyeno Esau anati: “Chabwino, ndiye ndikupatseko ena mwa anyamata angawa kuti akuthandize.” Koma iye anati: “Ayi musachite kutero. Musavutike mbuyanga,+ ndiyenda bwinobwino.” Miyambo 18:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Mphatso ya munthu imam’tsegulira khomo lalikulu,+ ndipo imakam’fikitsa ngakhale pamaso pa anthu olemekezeka.+
5 Tsopano ndili ndi ng’ombe, abulu, nkhosa, komanso antchito aamuna ndi aakazi.+ Ndatumiza amithenga kwa mbuyanga kukupemphani kuti mundikomere mtima.”’”+
15 Ndiyeno Esau anati: “Chabwino, ndiye ndikupatseko ena mwa anyamata angawa kuti akuthandize.” Koma iye anati: “Ayi musachite kutero. Musavutike mbuyanga,+ ndiyenda bwinobwino.”
16 Mphatso ya munthu imam’tsegulira khomo lalikulu,+ ndipo imakam’fikitsa ngakhale pamaso pa anthu olemekezeka.+