Genesis 30:43 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 43 Chuma cha Yakobo chinapitirira kuwonjezeka. Iye anakhala ndi ziweto zambiri, antchito aakazi ndi aamuna, ngamila ndi abulu.+ Genesis 33:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Chonde, landirani mphatso yokufunirani mafuno abwinoyi kuchokera kwa ine,+ chifukwa Mulungu wandikomera mtima, ndipo wandipatsa chilichonse.”+ Anamuumirizabe mpaka analandira mphatsoyo.+
43 Chuma cha Yakobo chinapitirira kuwonjezeka. Iye anakhala ndi ziweto zambiri, antchito aakazi ndi aamuna, ngamila ndi abulu.+
11 Chonde, landirani mphatso yokufunirani mafuno abwinoyi kuchokera kwa ine,+ chifukwa Mulungu wandikomera mtima, ndipo wandipatsa chilichonse.”+ Anamuumirizabe mpaka analandira mphatsoyo.+