Genesis 32:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Tsopano ndili ndi ng’ombe, abulu, nkhosa, komanso antchito aamuna ndi aakazi.+ Ndatumiza amithenga kwa mbuyanga kukupemphani kuti mundikomere mtima.”’”+ Genesis 36:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Iye anachoka chifukwa chuma chawo chinali chitawachulukira kwambiri, moti sakanathanso kukhala limodzi. Dziko lachilendo limene anali kukhalalo linali litawachepera chifukwa cha kuchuluka kwa ziweto zawo.+
5 Tsopano ndili ndi ng’ombe, abulu, nkhosa, komanso antchito aamuna ndi aakazi.+ Ndatumiza amithenga kwa mbuyanga kukupemphani kuti mundikomere mtima.”’”+
7 Iye anachoka chifukwa chuma chawo chinali chitawachulukira kwambiri, moti sakanathanso kukhala limodzi. Dziko lachilendo limene anali kukhalalo linali litawachepera chifukwa cha kuchuluka kwa ziweto zawo.+