Genesis 36:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Iye anachoka chifukwa chuma chawo chinali chitachuluka kwambiri, moti sakanathanso kukhala limodzi. Mʼdziko limene ankakhalalo* malo anali ochepa chifukwa ziweto zawo zinali zambiri.
7 Iye anachoka chifukwa chuma chawo chinali chitachuluka kwambiri, moti sakanathanso kukhala limodzi. Mʼdziko limene ankakhalalo* malo anali ochepa chifukwa ziweto zawo zinali zambiri.