Genesis 36:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Iye anachoka chifukwa chuma chawo chinali chitawachulukira kwambiri, moti sakanathanso kukhala limodzi. Dziko lachilendo limene anali kukhalalo linali litawachepera chifukwa cha kuchuluka kwa ziweto zawo.+
7 Iye anachoka chifukwa chuma chawo chinali chitawachulukira kwambiri, moti sakanathanso kukhala limodzi. Dziko lachilendo limene anali kukhalalo linali litawachepera chifukwa cha kuchuluka kwa ziweto zawo.+