Genesis 13:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Choncho, chifukwa chokhala ndi katundu wambiri, malo anawachepera moti sakanatha kukhala limodzi.+ Genesis 28:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Adzakupatsa iwe ndi mbewu zako+ madalitso amene analonjeza Abulahamu,+ kuti udzakhale mwini dziko limene ukukhalamo ngati mlendo,+ limene Mulungu anapatsa Abulahamu.”+
4 Adzakupatsa iwe ndi mbewu zako+ madalitso amene analonjeza Abulahamu,+ kuti udzakhale mwini dziko limene ukukhalamo ngati mlendo,+ limene Mulungu anapatsa Abulahamu.”+