Genesis 33:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Chonde landirani mphatso yangayi, yomwe ndabweretsa pokufunirani mafuno abwino,+ chifukwa Mulungu wandikomera mtima ndipo wandipatsa chilichonse.”+ Yakobo anapitiriza kumukakamiza mpaka analandira mphatsoyo.
11 Chonde landirani mphatso yangayi, yomwe ndabweretsa pokufunirani mafuno abwino,+ chifukwa Mulungu wandikomera mtima ndipo wandipatsa chilichonse.”+ Yakobo anapitiriza kumukakamiza mpaka analandira mphatsoyo.