Genesis 32:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Tsiku limeneli Yakobo anagona pamalopo. Kenako pa chuma chake anapatulapo zinthu zoti akapatse m’bale wake Esau ngati mphatso.+ Miyambo 18:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Mphatso ya munthu imam’tsegulira khomo lalikulu,+ ndipo imakam’fikitsa ngakhale pamaso pa anthu olemekezeka.+
13 Tsiku limeneli Yakobo anagona pamalopo. Kenako pa chuma chake anapatulapo zinthu zoti akapatse m’bale wake Esau ngati mphatso.+
16 Mphatso ya munthu imam’tsegulira khomo lalikulu,+ ndipo imakam’fikitsa ngakhale pamaso pa anthu olemekezeka.+