Genesis 30:43 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 43 Chuma cha Yakobo chinapitirira kuwonjezeka. Iye anakhala ndi ziweto zambiri, antchito aakazi ndi aamuna, ngamila ndi abulu.+ Aheberi 13:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Moyo wanu ukhale wosakonda ndalama,+ koma mukhale okhutira+ ndi zimene muli nazo pa nthawiyo.+ Pakuti Mulungu anati: “Sindidzakusiyani kapena kukutayani ngakhale pang’ono.”+
43 Chuma cha Yakobo chinapitirira kuwonjezeka. Iye anakhala ndi ziweto zambiri, antchito aakazi ndi aamuna, ngamila ndi abulu.+
5 Moyo wanu ukhale wosakonda ndalama,+ koma mukhale okhutira+ ndi zimene muli nazo pa nthawiyo.+ Pakuti Mulungu anati: “Sindidzakusiyani kapena kukutayani ngakhale pang’ono.”+