Genesis 35:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Zitatero, Mulungu anauza Yakobo kuti: “Nyamuka, pita ku Beteli ukakhale kumeneko.+ Ukamangire guwa lansembe Mulungu woona, amene anaonekera kwa iwe pamene unali kuthawa Esau m’bale wako.”+ Genesis 35:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Anamanga guwa lansembe kumeneko, n’kutchula malowo kuti Eli-beteli.* Malowo anawatcha dzinali chifukwa Mulungu woona anaonekera kwa iye kumeneko, pa nthawi imene anali kuthawa m’bale wake.+
35 Zitatero, Mulungu anauza Yakobo kuti: “Nyamuka, pita ku Beteli ukakhale kumeneko.+ Ukamangire guwa lansembe Mulungu woona, amene anaonekera kwa iwe pamene unali kuthawa Esau m’bale wako.”+
7 Anamanga guwa lansembe kumeneko, n’kutchula malowo kuti Eli-beteli.* Malowo anawatcha dzinali chifukwa Mulungu woona anaonekera kwa iye kumeneko, pa nthawi imene anali kuthawa m’bale wake.+