Genesis 35:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Anamanga guwa lansembe kumeneko nʼkutchula malowo kuti Eli-beteli.* Malowo anawapatsa dzinali chifukwa Mulungu woona anaonekera kwa iye kumeneko pamene ankathawa mʼbale wake.+
7 Anamanga guwa lansembe kumeneko nʼkutchula malowo kuti Eli-beteli.* Malowo anawapatsa dzinali chifukwa Mulungu woona anaonekera kwa iye kumeneko pamene ankathawa mʼbale wake.+