Genesis 35:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Anamanga guwa lansembe kumeneko, n’kutchula malowo kuti Eli-beteli.* Malowo anawatcha dzinali chifukwa Mulungu woona anaonekera kwa iye kumeneko, pa nthawi imene anali kuthawa m’bale wake.+
7 Anamanga guwa lansembe kumeneko, n’kutchula malowo kuti Eli-beteli.* Malowo anawatcha dzinali chifukwa Mulungu woona anaonekera kwa iye kumeneko, pa nthawi imene anali kuthawa m’bale wake.+