Salimo 37:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Usapse mtima ndipo pewa kukwiya.+Usapse mtima kuti ungachite choipa.+ Yakobo 1:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 chifukwa mkwiyo wa munthu subala chilungamo cha Mulungu.+